1 Samuel 10:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Atakupatsa moni, akuninkhako mitanda iŵiri ya buledi, iwe uilandire.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Iwowa adzakupatsani moni, ndi kukupatsani mikate iwiri; imeneyi mudzailandira m'manja mwao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Adzakupatsa moni ndi kukupatsa malofu awiri a buledi. Iwe udzalandire bulediyo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Iwowa adzakulankhulani, ndi kukupatsani mikate iwiri; imeneyi mudzailandira m'manja mwao.