1 Samuel 10:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono ukaona zizindikiro zimenezi, uchite chilichonse choyenera nthaŵi imeneyo, poti Mulungu ali nawe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo zitakufikirani zizindikiro izi mudzachita monga mudzaona pochita, pakuti Mulungu ali nanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Zizindikiro izi zikakachitika, dzachite chilichonse manja ako angathe kuchita, pakuti Mulungu ali nawe.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo zitakufikirani zizindikilo izi mudzacita monga mudzaona pocita, pakuti Mulungu ali nanu.