1 Samuel 11:10 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nchifukwa chake adauza Nahasi kuti, “Maŵa tidzadzipereka kwa inu, ndipo mutichite chilichonse chimene chikukomereni.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa chake anthu a ku Yabesi anati, Mawa tidzatulukira kwa inu, ndipo mudzatichitira chokomera inu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho anthu a ku Yabesi anawuza Nahasi kuti, “Mawa tidzadzipereka kwa inu ndipo inu mudzachite nafe chilichonse chokukomerani.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa cace anthu a ku Yabezi anati, Mawa tidzaturukira kwa inu, ndipo mudzaticitira cokomera inu.