1 Samuel 11:12 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Apo anthu adamufunsa Samuele kuti, “Ndani amene ankanena kuti, ‘Kodi Saulo nkutilamulira ife?’ Bwera nawoni anthuwo kuti tiŵaphe.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anthu anati kwa Samuele, Ndani iye amene anati, Kodi Saulo adzatiweruza ife? Tengani anthuwo kuti tiwaphe.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kenaka anthu anafunsa Samueli kuti, “Kodi ndani aja ankanena kuti, ‘Kodi Sauli nʼkutilamulira ife?’ Bwera nawoni kuno kuti tidzawaphe.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anthu anati kwa Samueli, Ndani iye amene anati, Kodi Sauli adzatiweruza ife? tengani anthuwo kuti tiwaphe.