1 Samuel 11:14 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono Samuele adauza anthuwo kuti, “Tiyeni tipite ku Giligala, tikatsimikizenso ufumu wa Saulo kumeneko.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Samuele ananena kwa anthuwo, Tiyeni tipite ku Giligala, kukonzanso ufumu kumeneko.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo Samueli anati kwa anthuwo, “Tiyeni tipite ku Giligala kuti tikatsimikizenso kuti Sauli ndi mfumu yathu.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Samueli ananena kwa anthuwo, Tiyeni tipite ku Giligala, kukonzanso ufumu kumeneko.