1 Samuel 12:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nchifukwa chake tsono imani pomwepa, kuti tikumbutsane pamaso pa Chauta za ntchito zonse zimene Iye adachita pokupulumutsani inu ndi makolo anu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa chake tsono, imani pano, kuti ndiweruzane nanu pamaso pa Yehova, anakuchitirani inu ndi makolo anu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nʼchifukwa chake tsopano imani pomwepa kuti ndikufotokozereni pamaso pa Yehova, za ntchito za chipulumutso zimene Yehova anachitira inu ndi makolo anu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa cace tsono, imani pano, kuti ndiweruzane nanu pamaso pa Yehova za nchito zonse zolungama za Yehova, anakucitirani inu ndi makolo anu.