1 Samuel 14:16 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Alonda a Saulo a ku Gibea ku dziko la Benjamini poti ayang'ane, adangoona chigulu cha adani chikumwazikira uku ndi uku.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ozonda a Saulo ku Gibea wa ku Benjamini anayang'ana; ndipo, onani, khamu la anthu linamwazikana, kulowa kwina ndi kwina.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Alonda a Sauli a ku Gibeya dziko la Benjamini atangomwaza maso anangoona chigulu cha asilikali chikumwazikana uku ndi uku.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ozonda a Sauli ku Gibeya wa ku Benjamini anayang'ana; ndipo, onani, khamu la anthu linamwazikana, kulowa kwina ndi kwina.