1 Samuel 14:18 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Apo Saulo adauza Ahiya kuti, “Bwera nayo kuno efodiyo.” Nthaŵi imeneyo efodiyo inali ndi Ahiya pamaso pa Aisraele.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Saulo ananena ndi Ahiya, Bwera nalo likasa la Mulungu kuno. Pakuti likasa la Mulungu linali kumeneko masiku aja ndi ana a Israele.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsono Sauli anawuza Ahiya kuti, “Bwera nalo Bokosi la Mulungulo.” (Nthawi imeneyo nʼkuti efodiyo ili ndi Ahiya pamaso pa Aisraeli).
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Sauli ananena ndi Ahiya, Bwera nalo likasa la Mulungu kuno. Pakuti likasa la Mulungu linali kumeneko masiku aja ndi ana a Israyeli.