1 Samuel 14:31 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsikulo Aisraele adapha Afilisti kuyambira ku Mikimasi mpaka ku Ayaloni. Koma Aisraelewo anali pafupi kukomoka nayo njala.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anakantha Afilisti tsiku lija kuyambira ku Mikimasi kufikira ku Ayaloni, ndipo anthu anafooka kwambiri.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsiku limenelo Aisraeli anapha Afilisti kuchokera ku Mikimasi mpaka ku Ayaloni. Koma Aisraeliwo analefuka kwambiri ndi njala.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anakantha Afilisti tsiku lija kuyambira ku Mikimasi kufikira ku Ajaloni, ndipo anthu anafoka kwambiri.