1 Samuel 14:42 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono Saulo adati, “Chitani maere pakati pa ine ndi mwana wanga Yonatani.” Ndipo maere adagwera Yonatani.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Saulo anati, Muchite maere pakati pa ine ndi Yonatani mwana wanga. Ndipo anagwera Yonatani.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Sauli anati, “Chitani maere pakati pa ine ndi Yonatani mwana wanga.” Ndipo maere anagwera Yonatani.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Sauli anati, Mucite maere pakati pa ine ndi Jonatani mwana wanga. Ndipo anagwera Jonatani.