1 Samuel 14:49 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ana aamuna a Saulo anali Yonatani, Isivi ndi Malikisuwa. Analinso ndi ana aŵiri aakazi, wamkulu anali Merabi, wamng'ono anali Mikala.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ana a Saulo ndiwo Yonatani, ndi Isivi, ndi Malikisuwa; ndi maina a ana akazi ake awiri ndi awa: dzina la woyamba ndiye Merabi, ndi dzina la mng'ono wake ndiye Mikala;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ana aamuna a Sauli anali Yonatani, Isivi ndi Maliki-Suwa. Analinso ndi ana aakazi awiri, dzina la mwana wake wamkulu wamkazi linali Merabi ndipo la mwana wake wamngʼono wamkazi linali Mikala.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ana a Sauli ndiwo Jonatani, ndi Isivi, ndi Malikisuwa; ndi maina a ana akazi ace awm ndi awa: dzina la woyamba ndiye Merabu, ndi dzina la mng'ono wace ndiye Mikala;