1 Samuel 14:52 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pa moyo wake wonse Saulo ankakhalira kuchita nkhondo ndi Afilisti. Tsono ankati akaona munthu wamphamvu kapena wolimba mtima, ankamulemba m'gulu lake lankhondo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo panali nkhondo yowawa ndi Afilisti masiku onse a Saulo; ndipo Saulo pakuona munthu wamphamvu, kapena ngwazi, anamtenga akhale naye.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pa moyo wake wonse, Sauli ankakhalira kuchita nkhondo pakati pa Israeli ndi Afilisti. Ndipo Sauli ankati akaona munthu aliyense wamphamvu kapena wolimba mtima ankamulemba ntchito mu gulu lake lankhondo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo panali nkhondo yowawa ndi Afilisti masiku onse a Sauli; ndipo Sauli pakuona munthu wamphamvu, kapena ngwazi, anamtenga akhale naye.