1 Samuel 14:8 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono Yonatani adati, “Tiwolokere kwa anthuwo, ndipo tikadziwonetse kwa iwo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Yonatani anati, Taona, ife tidzapita kunka kwa anthuwo, ndipo tidzadziwulula kwa iwo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yonatani anati, “Tiye tsono tiwoloke kupita kumene kuli anthuwo ndi kukadzionetsa kwa iwo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Jonatani anati, Taona, ife tidzapita kunka kwa anthuwo, ndipo tidzadziu lula kwa iwo.