1 Samuel 15:14 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma Samuele adati, “Nanga bwanji ndikumva nkhosa ndi ng'ombe zikulira?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Samuele anati, Koma tsono kulirako kwa nkhosa ndilikumva m'makutu anga, ndi kulirako kwa ng'ombe ndilikumva, nchiyani?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma Samueli anati, “Nanga bwanji ndikumva kulira kwa nkhosa ndi ngʼombe?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Samueli anati, Koma tsono kulirako kwa nkhosa ndirikumva m'makutu anga, ndi kulirako kwa ng'ombe ndirikumva, nciani?