1 Samuel 15:19 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chifukwa chiyani nanga simudamvere mau a Chauta? Chifukwa chiyani mudathamangira zofunkha ndi kuchita zoipira Chauta?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa ninji tsono simunamvera mau a Yehova, koma munathamangira zowawanya, ndi kuchita choipa pamaso pa Yehova?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chifukwa chiyani simunamvere mawu a Yehova? Chifukwa chiyani munathamangira zofunkha ndi kuchita choyipira Yehova?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa ninji tsono simunamvera mau a Yehova, koma munathamangira zowawanya, ndi kucita coipa pamaso pa Yehova?