1 Samuel 15:34 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono Samuele adapita ku Rama, koma Saulo adapita ku nyumba yake ku Gibea wa Saulo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo Samuele ananka ku Rama; ndi Saulo anakwera kunka kunyumba yake ku Gibea wa Saulo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo Samueli anapita ku Rama, koma Sauli anapita ku mudzi kwawo ku Gibeya wa Sauli.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo Samueli ananka ku Rama; ndi Sauli anakwera kunka ku nyumba yace ku Gibeya wa Sauli.