1 Samuel 15:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo Saulo adafika ku mzinda wa Aamaleke, naubisalira m'khwaŵa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Saulo anafika kumudzi wa Amaleke, nalalira kuchigwa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Sauli anapita ku mzinda wa Aamaleki nawubisalira mʼkhwawa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Sauli anafika ku mudzi wa Amaleki, nalalira kucigwa.