1 Samuel 15:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamenepo Saulo adagonjetsa Aamaleke kuyambira ku Havila mpaka ku Suri, kuvuma kwa Ejipito.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Saulo anakantha Aamaleke, kuyambira pa Havila, dera la ku Suri, chili pandunji pa Ejipito.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsono Sauli anakantha Aamaleki kuchokera ku Havila mpaka ku Suri, kummawa kwa Igupto.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Sauli anakantha Aamaleki, kuyambira pa Havila, dera la ku Suri; ciri pandunji pa Aigupto.