1 Samuel 15:8 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adamtenga wamoyo Agagi, mfumu ya Aamaleke, ndipo adapha anthu ena onse ndi lupanga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Namtenga wamoyo Agagi, mfumu ya Aamaleke, naononga konsekonse anthu onse ndi lupanga lakuthwa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Sauli anatenga Agagi mfumu ya Aamaleki, koma anthu ake onse anawapha ndi lupanga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Namtenga wamoyo Agagi, mfumu ya Aamaleki, naononga konse konse anthu onse ndi lupanga lakuthwa.