1 Samuel 16:15 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Atumiki ake adamuuza kuti, “Onani, tsopano mzimu woipa, wotumidwa ndi Mulungu, ukukuzunzani.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anyamata a Saulo ananena naye, Onani tsopano, mzimu woipa wochokera kwa Mulungu ulikuvuta inu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Atumiki a Sauli anati, “Taonani mzimu woyipa wochokera kwa Mulungu ukukuzunzani.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anyamata a Sauli ananena naye, Onani tsopano, mzimu woipa wocokera kwa Mulungu ulikubvuta inu.