1 Samuel 16:19 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Choncho Saulo adatuma amithenga kwa Yese kukanena kuti, “Tumizire Davide mwana wako, uja amaŵeta nkhosayu.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa chake Saulo anatumiza mithenga kwa Yese, nati, Unditumizire Davide, mwana wako, amene ali kunkhosa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo Sauli anatumiza amithenga kwa Yese kukanena kuti, “Nditumizireni mwana wanu Davide, amene amaweta nkhosa.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa cace Sauli anatumiza mithenga kwa Jese, nati, Vnditumizire Davide, mwana wako, amene ali kunkhosa.