1 Samuel 16:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Samuele adafunsa Chauta kuti, “Kodi ndingathe bwanji kupitako? Saulo akamva zimenezi, adzandipha.” Chauta adati, “Utenge ng'ombe yaikazi popita, ndipo ukanene kuti, ‘Ndadzapereka nsembe kwa Chauta.’
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Samuele anati, Ndikamuka bwanji? Saulo akachimva, adzandipha. Ndipo Yehova anati, Umuke nayo ng'ombe yaikazi, nunene kuti, Ndadza kudzaphera nsembe kwa Yehova.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma Samueli anati, “Kodi ndingapite bwanji? Sauli akamva zimenezi adzandipha.” Yehova anayankha, “Tenga ngʼombe yayikazi ndipo ukanene kuti, ‘Ndabwera kudzapereka nsembe kwa Yehova.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Samueli anati, Ndikamuka bwanji? Sauli akacimva, adzandipha. Ndipo Yehova anati, Umuke nayo ng'ombe yaikazi, nunene kuti, Ndadza kudzaphera nsembe kwa Yehova.