1 Samuel 16:22 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kenaka Saulo adatumiza mau kwa Yese kuti, “Davide akhale womanditumikira, pakuti ndamkonda kwambiri.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Saulo anatumiza kwa Yese, nati, Ulole kuti Davide aime pamaso panga; pakuti ndamkomera mtima.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kenaka Sauli anatumiza mawu kwa Yese ndi kuti, “Mulole kuti Davide azinditumikira, pakuti ndamukonda kwambiri.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Sauli anatumiza kwa Jese, nati, Ulole kuti Davide aime pamaso panga; pakuti ndamkomera mtima.