1 Samuel 16:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Onsewo atafika, Samuele adayang'ana Eliyabu namaganiza kuti, “Ndithudi amene Chauta adamsankha ndi uyu ali pamaso pakeyu.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo kunali, pakufika iwo, iye anayang'ana pa Eliyabu, nati, Zoonadi, wodzozedwa wa Yehova ali pamaso pake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamene anafika, Samueli anaona Eliabu ndipo anaganiza “Ndithu wodzozedwa wa Yehova uja ndi uyu wayima pamaso pakeyu.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo kunali, pakufika iwo, iye anayang'ana pa Eliyabu, nati, Zoonadi, wodzozedwa wa Yehova ali pamaso pace.