1 Samuel 17:24 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Aisraele onse atamuwona munthuyo, adathaŵa chifukwa ankamuwopa kwambiri.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Aisraele onse, pakumuona munthuyo, anamthawa, naopa kwambiri.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Aisraeli ataona munthuyo, anamuthawa ndi mantha aakulu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Aisrayeli onse, pakumuona munthuyo, anamthawa, naopa kwambiri.