1 Samuel 17:32 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono Davide adauza Saulo kuti, “Munthu aliyense asataye mtima chifukwa cha Mfilistiyu. Ineyo mnyamata wanune ndipita kukamenyana naye.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Davide anati kwa Saulo, Asade nkhawa munthu aliyense chifukwa cha iyeyo; ine kapolo wanu ndidzapita kuponyana ndi Mfilisti uyu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Davide anati kwa Sauli, “Munthu aliyense asataye mtima chifukwa cha Mfilisitiyu. Ine kapolo wanu ndipita kukamenyana naye.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Davide anati kwa Sauli, Asade nkhawa munthu ali yense cifukwa ca iyeyo; ine kapolo wanu ndidzapita kuponyana ndi Mfilisti uyu.