1 Samuel 17:33 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Saulo adamuuza kuti, “Sungathe kukamenyana naye Mfilistiyu, pakuti iwe ndiwe mnyamata, koma iyeyu ndi munthu wozoloŵera kumenya nkhondo kuyambira ubwana wake.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Saulo anati kwa Davide, Sukhoza iwe kukomana ndi Mfilisti uyu kukaponyana naye; pakuti iwe ndiwe mnyamata, koma iye anazolowera nkhondo kuyambira ubwana wake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Sauli anayankha Davide kuti, “Iwe sungathe kupita kukamenyana ndi Mfilisitiyu. Iwe ukanali mnyamata, koma iyeyu ndi amene wakhala akumenya nkhondo kuyambira unyamata wake.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Sauli anati kwa Davide, Sukhoza iwe kukomana ndi Mfilisti uyu kukaponyana naye; pakuti iwe ndiwe mnyamata, koma iye anazolowera nkhondo kuyambira ubwana wace.