1 Samuel 17:44 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kenaka adauza Davide kuti, “Idza kuno, mnofu wako ndidyetsera mbalame zamumlengalenga ndi zilombo zakuthengo.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Mfilistiyo anati kwa Davide, Idza kuno kwa ine, ndidzapatsa mnofu wako kwa mbalame za mlengalenga, ndi kwa zilombo za kuthengo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye anatinso, “Bwera kuno ndipo ndidzapereka mnofu wako kwa mbalame zamlengalenga ndi kwa zirombo zakuthengo!”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Mfilistiyo anati kwa Davide, Idza kuno kwa ine, ndidzapatsa mnofu wako kwa mbalame za mlengalenga, ndi kwa zirombo za kuthengo.