1 Samuel 17:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ankavala chisoti chamkuŵa ndi malaya achitsulo, amene kulemera kwake kunali ngati makilogramu 57.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anali ndi chisoti chamkuwa pamutu pake, navala malaya aunyolo, olemera ngati masekeli zikwi zisanu za mkuwa,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye ankavala chipewa chamkuwa ndi malaya achitsulo olemera makilogalamu 57.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anali ndi cisoti camkuwa pamutu pace, nabvala maraya aunyolo, olemera ngati masekeli zikwi zisanu za mkuwa,