1 Samuel 17:56 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Apo mfumu idati, “Kafunse kuti kodi mnyamata ameneyu ndi mwana wa yani?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo mfumu inati, Ufunsire kuti mnyamatayo ndi mwana wa yani.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mfumu inati, “Pita kafufuze kuti mnyamata ameneyu ndi mwana wa yani.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo mfumu inati, Ufunsire kuti mnyamatayo ndi mwana wa yani.