1 Samuel 17:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ankavalanso zokuta miyendo yake zamkuŵa, ndipo ankanyamula nthungo yamkuŵa pa phewa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
nakuta msongolo wake ndi chovala chamkuwa, ndiponso pachikota pake panali nthungo yamkuwa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ankavalanso zokuta miyendo yake zamkuwa, ndipo ankanyamula nthungo ya mkuwa pa phewa pake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
nakuta msongolo wace ndi cobvala camkuwa, ndiponso pacikota pace panali nthungo yamkuwa.