1 Samuel 18:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pambuyo pake Saulo adayamba kuwopa Davide, chifukwa choti tsopano Chauta anali ndi Davide, kumsiya iyeyo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Saulo anaopa Davide chifukwa Yehova anali naye, koma adamchokera Saulo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pambuyo pake Sauli amamuopa Davide chifukwa Yehova anali ndi Davideyo, nʼkumusiya Sauli.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Sauli anaopa Davide, cifukwa Yehova anali naye, koma adamcokera Sauli.