1 Samuel 18:15 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono pamene Saulo adaona kuti Davide akupambana kwambiri, adayamba kuchita naye mantha.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo pamene Saulo anaona kuti analikukhala wochenjera ndithu anamuopa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Sauli ataona momwe Davide ankapambanira, iye anamuopa kwambiri.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo pamene Sauli anaona kuti analikukhala wocenjera ndithu anamuopa.