1 Samuel 18:29 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
adamuwopabe kwambiri ndi kudana naye moyo wake wonse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Saulo nayamba kumuopa Davide kopambana; ndi Saulo anali mdani wa Davide masiku onse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
iye anapitirirabe kumuopa Davide ndi kumadana naye moyo wake wonse.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Sauli nayamba kumuopa Davide kopambana; ndi Sauli anali mdani wa Davide masiku onse.