1 Samuel 18:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adachita naye chipangano chifukwa ankamkonda monga momwe ankadzikondera iye mwini.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo Yonatani ndi Davide anapangana pangano, pakuti adamkonda iye ngati moyo wa iye yekha.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo Yonatani anapanga pangano ndi Davide chifukwa ankamukonda monga momwe ankadzikondera.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo Jonatani ndi Davide anapangana pangano, pakuti adamkonda iye ngati moyo wa iye yekha.