1 Samuel 18:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Akaziwo ankapolokezana akukondwerera namati, “Saulo wapha zikwi inde, koma Davide wapha zikwi khumikhumi!”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo akazi anathirirana mang'ombe m'kuimba kwao, nati, Saulo anapha zikwi zake, koma Davide zikwi zake zankhani.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Amayiwo ankalandizana nyimbo mokondwera namati: “Sauli wapha 1,000, Koma Davide wapha miyandamiyanda.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo akazi anathirirana mang'ombe m'kuyimba kwao, nati, Sauli anapha zikwi zace, Koma Davide zikwi zace zankhani.