1 Samuel 18:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Apo Saulo adapsa mtima kwambiri, mau ameneŵa adaipidwa nawo. Adati, “Davide amuŵerengera zikwi zochuluka, koma ine andiŵerengera zikwi zochepa. Nanga chamkhaliranso nchiyani? Si ufumu basi?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma Saulo anakwiya ndithu, ndi kunenaku kunamuipira; nati, Kwa Davide anawerengera zikwi zankhani, koma kwa ine zikwi zokha; chimperewera nchiyaninso, koma ufumu wokha?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma Sauli anapsa mtima kwambiri ndipo mawu amenewa anamuyipira. Iye anati, “Iwo amuwerengera Davide miyandamiyanda, koma ine 1,000 okha. Nanga chatsalanso nʼchiyani kuti atenge? Si ufumu basi?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma Sauli anakwiya ndithu, ndi kunenaku kunamuipira; nati, Kwa Davide anawereogera zikwi zankhani, koma kwa ine zikwi zokha; cimperewera ncianioso, koma ufumu wokha?