1 Samuel 19:14 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamene anthu a Saulo aja adafika kuti adzamgwire Davide, Mikala adati, “Davide akudwala.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo pamene Saulo anatumiza mithenga kuti ikamgwire Davide, anati, Iye alikudwala.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamene amithenga a Sauli aja anafika kuti akamugwire Davide, Mikala anati, “Davide akudwala.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo pamene Sauli anatumiza mithenga kuti ikamgwire Davide, anati, iye alikudwala.