1 Samuel 2:18 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Samuele pa unyamata wake ankatumikira pamaso pa Chauta, atavala efodi yabafuta.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma Samuele anatumikira pamaso pa Yehova akali mwana, atamangira m'chuuno ndi efodi wabafuta.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma Samueli amatumikira pamaso pa Yehova atavala efodi ya nsalu yofewa yosalala.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma Samueli anatumikira pamaso pa Yehova akali mwana, atamangira m'cuuno ndi efodi wabafuta.