1 Samuel 2:24 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Iyai ana anga, zimene ndilikumva anthu a Chauta akusimba nkumafalitsa, si zabwino ai.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Iai, ana anga, popeza mbiri imene ndilikuimva sili yabwino iai; mulikulakwitsa anthu a Yehova.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ayi, ana anga si mbiri yabwino imene ndikumva anthu a Mulungu akufalitsa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Iai, ana anga, popeza mbiri imene ndirikuimva siri yabwino iai; mulikulakwitsa anthu a Yehova.