1 Samuel 2:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ankhondo amphamvu mauta ao athyoka, koma anthu ofooka avala dzilimbe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mauta a amphamvu anathyoka, koma okhumudwawo amangiridwa ndi mphamvu m'chuuno.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Mauta a anthu ankhondo athyoka koma anthu ofowoka avala dzilimbe.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mauta a amphamvu anathyoka, Koma okhumudwawo amangiridwa ndi mphamvu m'cuuno.