1 Samuel 2:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu amene kale adaali okhuta, tsopano akusuma, koma amene kale adaali ndi njala, tsopano akukhuta. Chumba chabala ana asanu ndi aŵiri, koma wobereka ana ambiri watsala yekha.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Amene anakhuta anakasuma chakudya; koma anjalawo anachira; inde chumba chabala asanu ndi awiri; ndipo iye amene ali ndi ana ambiri achita liwondewonde.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Amene kale anali okhuta tsopano akukagula chakudya, koma iwo amene anali ndi njala sakumvanso njala. Amene anali wosabereka, wabereka ana aamuna asanu ndi awiri, koma iye wobereka ana ambiri watsala yekha.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Amene anakhuta anakasuma cakudya; Koma anjalawo anacira; Inde cumba cabala asanu ndi awiri: Ndipo iye amene ali ndi ana ambiri acita liwondewonde.