1 Samuel 2:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Anthu okhulupirika Iye adzatchinjiriza moyo wao, koma anthu oipa adzazimirira mu mdima, pakuti munthu sapambana ndi mphamvu zake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Adzasunga mapazi a okondedwa ake, koma oipawo adzawakhalitsa chete mumdima; pakuti palibe munthu adzapambana ndi mphamvu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye adzateteza moyo wa anthu okhulupirika koma anthu oyipa adzawonongedwa mu mdima. “Pakuti munthu sapambana ndi mphamvu zake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Adzasunga mapazi a okoodedwaace, Koma oipawo adzawakhalitsa cete mumdima; Pakuti palibe munthu adzapambana ndi mphamvu,