1 Samuel 20:11 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Yonatani adayankha kuti, “Tiye tikayende chakumindaku.” Choncho onse aŵiriwo adapita kumeneko.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nati Yonatani kwa Davide, Tiyeni timuke kuthengo. Namuka onse awiri kuthengoko.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yonatani anawuza Davide kuti, “Tiyeni tikayende ku mundako.” Ndipo anapita onse awiri.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nati Jonatani kwa Davide, Tiyeni timuke kuthengo. Namuka onse awiri kuthengoko.