1 Samuel 20:14 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndikakhala ndili moyobe, udzandiwonetse kukoma mtima konga kwa Chauta. Koma ndikafa, usadzaleke kuchitira chifundo banja langa mpaka muyaya.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo undionetsere chifundo cha Yehova, si pokhala ine ndi moyo pokha, kuti ndingafe;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndikakhalabe ndi moyo udzandionetse kukoma mtima monga kwa Yehova nthawi yonse ya moyo wanga, kuti ine ndisaphedwe.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo undionetsere cifundo ca Yehova, si pokhala ine ndi moyo pokha, kuti ndingafe;