1 Samuel 20:15 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamene Chauta adzaŵatha adani onse a Davide pa dziko lapansi,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
komanso usaleke kuchitira chifundo a m'nyumba yanga nthawi zonse: mungakhale m'tsogolomo Yehova atathera adani onse a Davide pa dziko lapansi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo usadzaleke kuchitira chifundo banja langa. Pamene Yehova adzawatha adani onse a Davide pa dziko lapansi.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
komanso usaleke kucitira cifundo a m'nyumba yanga nthawi zonse; mungakhale m'tsogolomo Yehova atathera adani onse a Da vide pa dziko lapansi.