1 Samuel 20:19 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mkucha adzakufunanso kwambiri. Tsono udzapite ku malo amene udaabisala tsiku lijali, ndipo ukakhale pa mbali ina ya mulu wa miyala uli apowo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo atapita masiku atatu, utsike msanga, nufike kumene unabisala tsiku la mlandu uja, nukhale pa mwala wa Ezeri.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mkuja adzakufunafuna. Tsono udzapite pamalo pamene unabisala poyamba paja ndipo ukadikire pa mulu wa miyala uli apowo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo atapita masiku atatu, utsike msanga, nufike kumene unabisala tsiku la mrandu uja, nukhale pa mwala wa Ezeri.