1 Samuel 20:22 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma ndikamuuza mnyamatayo kuti, ‘Mivi ili patsogolo pako,’ pomwepo iweyo uchoke, pakuti Chauta ndiye wati uchokepo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma ndikati kwa mnyamatayo, Ona mivi ili kutsogoloko; pamenepo unyamuke ulendo wako; popeza Yehova wakuuza umuke.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma ndikadzati, ‘Taona mivi ili patsogolo pako,’ iwe udzachoke chifukwa Yehova ndiye walola kuti uchokepo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma ndikati kwa mnyamatayo, Ona mibvi iri kutsogoloko; pamenepo unyamuke ulendo wako; popeza Yehova wakuuza umuke.