1 Samuel 20:23 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono pa zimene tapanganazi, Chauta ndiye mboni pakati pa ine ndi iwe mpaka muyaya.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo za chija tinakambirana iwe ndi ine, taona, Yehova ali pakati pa ife nthawi zonse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsono zimene tapanganazi Yehova ndiye mboni pakati pa iwe ndi ine mpaka muyaya.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo za cija tinakambirana iwe ndi ine, taona, Yehova ali pakati pa ife nthawi zonse.