1 Samuel 20:32 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Yonatani adafunsa bambo wake kuti, “Kodi chifukwa chiyani mufuna kumupha Davide? Kodi walakwa chiyani?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Yonatani anayankha Saulo atate wake, nanena, Aphedwe chifukwa ninji? Anachitanji?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yonatani anafunsa abambo ake kuti, “Nʼchifukwa chiyani mufuna kuti Davide aphedwe? Iye walakwa chiyani?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Jonatani anayankha Sauli atate wace, nanena, Aphedwe cifukwa ninji? anacitanji?